Amosi 2:3 - Buku Lopatulika3 ndipo ndidzalikha woweruza pakati pake, ndi kupha akalonga ake onse, ati Yehova. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 ndipo ndidzalikha woweruza pakati pake, ndi kupha akalonga ake onse, ati Yehova. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Ndidzaŵaphera wolamulira wao, Ndidzaphanso nduna zake pamodzi naye.” Akuterotu Chauta. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Ndidzawononga wolamulira wake ndi kupha akuluakulu onse amene ali pamodzi ndi iye,” akutero Yehova. Onani mutuwo |