Amosi 2:2 - Buku Lopatulika2 koma ndidzatumiza moto pa Mowabu, udzanyeketsa nyumba zachifumu za Keriyoti; ndipo Mowabu adzafa ndi phokoso, ndi kufuula, ndi mau a lipenga; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 koma ndidzatumiza moto pa Mowabu, udzanyeketsa nyumba zachifumu za Keriyoti; ndipo Mowabu adzafa ndi phokoso, ndi kufuula, ndi mau a lipenga; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Nchifukwa chake Ineyo ndidzaponya moto ku Mowabu, ndipo motowo udzapsereza malinga a ku Keriyoti. Anthu a ku Mowabu adzafera pakati pa phokoso la nkhondo, asilikali akufuula ndi kuliza malipenga. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Ine ndidzatumiza moto pa Mowabu, umene udzanyeketsa nyumba zaufumu za ku Keriyoti. Mowabu adzafera pakati pa nkhondo yoopsa, mʼkati mwa mfuwu wa nkhondo ndi kuliza malipenga. Onani mutuwo |