Amosi 2:16 - Buku Lopatulika16 ndi wolimba mtima mwa ngwazi adzathawa wamaliseche tsiku lomwelo, ati Yehova. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 ndi wolimba mtima mwa ngwazi adzathawa wamaliseche tsiku lomwelo, ati Yehova. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Pa tsiku limenelo ngakhale wolimba mtima pakati pa anthu a mphamvu, adzathaŵa ali maliseche.” Akuterotu Chauta. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Ngakhale asilikali olimba mtima kwambiri adzathawa ali maliseche pa tsikulo,” akutero Yehova. Onani mutuwo |