Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Amosi 1:10 - Buku Lopatulika

10 koma ndidzatumiza moto pa linga la Tiro, ndipo udzanyeketsa nyumba zake zachifumu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

10 koma ndidzatumiza moto pa linga la Tiro, ndipo udzanyeketsa nyumba zake zachifumu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

10 Ndiye Ine ndidzaponya moto pa makoma ozinga Tiro, ndipo motowo udzatentha malinga ake.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

10 Ine ndidzatumiza moto pa makoma a Turo umene udzanyeketsa nyumba zake zaufumu.”

Onani mutuwo Koperani




Amosi 1:10
8 Mawu Ofanana  

chifukwa cha tsiku lakudzafunkha Afilisti onse, kuphera Tiro ndi Sidoni othangata onse akutsala; pakuti Yehova adzafunkha Afilisti, otsala a chisumbu cha Kafitori.


Ndipo adzalanda chuma chako ndi kufunkha malonda ako, nadzagwetsa malinga ako ndi kupasula nyumba zako zofunika, nadzaponya miyala yako, ndi mitengo yako, ndi fumbi lako, m'madzi.


Ndipo adzagumula malinga a Tiro, ndi kugwetsa nsanja zake; inde ndidzausesa fumbi lake, ndi kuuyesa pathanthwe poyera.


Mwa mphulupulu zako zochuluka ndi malonda ako osalungama waipsa malo ako opatulika; chifukwa chake ndatulutsa moto m'kati mwako wakunyeketsa iwe; ndipo ndakusandutsa mapulusa panthaka pamaso pa onse akuona.


Ndiponso ndili ndi chiyani ndi inu, Tiro ndi Sidoni, ndi malire onse a Filistiya? Mudzandibwezera chilango kodi? Mukandibwezera chilango msanga, mofulumira, ndidzabwezera chilango chanu pamutu panu.


koma ndidzatumiza moto kunyumba ya Hazaele, ndipo udzanyeketsa nyumba zachifumu za Benihadadi.


koma ndidzatumiza moto pa linga la Gaza, ndipo udzatha nyumba zake zachifumu;


Taonani, Ambuye adzamlanda zake, nadzakantha mphamvu yake igwe m'manja; ndipo adzatha ndi moto.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa