Akolose 4:8 - Buku Lopatulika8 amene ndamtuma kwa inu chifukwa cha ichi chomwe, kuti mukazindikire za kwa ife, ndi kuti atonthoze mitima yanu; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 amene ndamtuma kwa inu chifukwa cha ichi chomwe, kuti mukazindikire za kwa ife, ndi kuti atonthoze mitima yanu; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Nchifukwa chake ndikumtuma kwa inu kuti mudziŵe za m'mene tiliri, ndipo kuti adzakulimbitseni mtima. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Ine ndikumutumiza kwa inu ndi cholinga choti mudziwe zimene tikukumana nazo ndiponso kuti alimbikitse mitima yanu. Onani mutuwo |