Akolose 4:7 - Buku Lopatulika7 Zonse za kwa ine adzakuzindikiritsani Tikiko, mbale wokondedwa ndi mtumiki wokhulupirika ndi kapolo mnzanga mwa Ambuye: Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Zonse za kwa ine adzakuzindikiritsani Tikiko, mbale wokondedwa ndi mtumiki wokhulupirika ndi kapolo mnzanga mwa Ambuye: Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Tikiko, mbale wathu wokondedwa, adzakudziŵitsani zonse za ine. Iyeyo ndi mtumiki wokhulupirika, wantchito mnzathu pa ntchito ya Ambuye. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Tukiko adzakuwuzani zonse za ine. Iye ndi mʼbale wokondedwa, mtumiki wokhulupirika ndiponso wantchito mnzanga mwa Ambuye. Onani mutuwo |