Akolose 4:18 - Buku Lopatulika18 Ndipereka moni ndi dzanja langa, kwa ine Paulo. Kumbukirani zomangira zanga. Chisomo chikhale nanu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Ndipereka moni ndi dzanja langa, kwa ine Paulo. Kumbukirani zomangira zanga. Chisomo chikhale nanu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Ndi dzanja langalanga ndikulemba mau aŵa: “Moni. Ndine Paulo.” Kumbukirani kuti ndili m'maunyolo. Mulungu akukomereni mtima. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Ine Paulo, ndikulemba ndi dzanja langa moni uwu. Kumbukirani kuti ndili mu unyolo. Chisomo chikhale ndi inu. Onani mutuwo |