Akolose 3:9 - Buku Lopatulika9 musamanamizana wina ndi mnzake; popeza mudavula munthu wakale pamodzi ndi ntchito zake, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 musamanamizana wina ndi mnzake; popeza mudavula munthu wakale pamodzi ndi ntchito zake, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Musamauzana mabodza, pakuti mwachita ngati mwavula moyo wanu wakale, pamodzi ndi zochitachita zake zoipa, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Musanamizane wina ndi mnzake, popeza munavula munthu wakale pamodzi ndi zochita zake Onani mutuwo |