Akolose 3:4 - Buku Lopatulika4 Pamene Khristu adzaoneka, ndiye moyo wathu, pamenepo inunso mudzaonekera pamodzi ndi Iye mu ulemerero. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Pamene Khristu adzaoneka, ndiye moyo wathu, pamenepo inunso mudzaonekera pamodzi ndi Iye m'ulemerero. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Khristu ndiye moyo wanu weniweni tsopano, choncho pamene Iye adzaonekerenso, inunso mudzaonekera mu ulemerero pamodzi naye. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Khristu, amene ndiye moyo wanu, akadzaonekanso, pamenepo inunso mudzaoneka naye pamodzi mu ulemerero. Onani mutuwo |