Akolose 3:21 - Buku Lopatulika21 Atate inu, musaputa ana anu, kuti angataye mtima. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 Atate inu, musaputa ana anu, kuti angataye mtima. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Inu atate, musamaŵapsetsa mtima ana anu, kuti angataye mtima. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Inu abambo, musakwiyitse ana anu, kuti angataye mtima. Onani mutuwo |