Akolose 2:17 - Buku Lopatulika17 ndizo mthunzi wa zilinkudzazo; koma thupi ndi la Khristu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 ndizo mthunzi wa zilinkudzazo; koma thupi ndi la Khristu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 Zonsezi ndi chithunzithunzi chabe cha zinthu zenizeni zimene zilikudza, koma zenizenizo ndi Khristu amene. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 Zimenezi ndi chithunzithunzi chabe cha zinthu zimene zikubwera, koma choonadi chenicheni chikupezeka mwa Khristu. Onani mutuwo |