Akolose 1:26 - Buku Lopatulika26 ndiwo chinsinsicho chinabisika kuyambira pa nthawizo, ndi kuyambira pa mibadwoyo; koma anachionetsa tsopano kwa oyera mtima ake, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201426 ndiwo chinsinsicho chinabisika kuyambira pa nthawizo, ndi kuyambira pa mibadwoyo; koma anachionetsa tsopano kwa oyera mtima ake, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa26 Mauwo ndi chinsinsi chozama chimene chinali chobisika chikhalire kwa mibadwo yonse, koma tsopano Mulungu wachiwululira anthu ake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero26 chinsinsi chimene chakhala chikubisika kwa nthawi ndi mibado, koma tsopano chawululidwa kwa oyera mtima. Onani mutuwo |