Ahebri 9:25 - Buku Lopatulika25 kosati kuti adzipereke yekha kawirikawiri; monga mkulu wa ansembe alowa m'malo opatulika chaka ndi chaka ndi mwazi wosati wake; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201425 kosati kuti adzipereke yekha kawirikawiri; monga mkulu wa ansembe alowa m'malo opatulika chaka ndi chaka ndi mwazi wosati wake; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa25 Mkulu wa ansembe onse amaloŵa m'Malo Opatulika Kopambana chaka ndi chaka atatenga magazi amene sali ake. Koma Khristu sadaloŵe Kumwamba kuti azidzipereka nsembe kaŵirikaŵiri. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero25 Iye sanalowe kumwamba kuti azikadziperekanso nsembe kachiwiri monga momwe mkulu wa ansembe ankachitira chaka ndi chaka ku Malo Opatulika kwambiri ndi magazi amene sanali ake. Onani mutuwo |