Ahebri 9:21 - Buku Lopatulika21 Ndiponso chihema ndi zotengera zonse za utumikiro anaziwaza momwemo ndi mwaziwo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 Ndiponso chihema ndi zotengera zonse za utumikiro anaziwaza momwemo ndi mwaziwo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Momwemonso Mose adawaza magazi pa chihema ndi pa ziŵiya zonse zogwirira ntchito pa chipembedzo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Momwemonso Mose anawaza magazi pa Chihema chija ndiponso pa zipangizo zonse zogwiritsa ntchito pa chipembedzo. Onani mutuwo |
Pamenepo uiphe nkhosa yamphongoyo, nutapeko pa mwazi wake, ndi kuupaka pa ndewerere ya khutu lamanja la Aroni, ndi pa ndewerere ya khutu lamanja ana ake aamuna, ndi pa chala chachikulu cha dzanja lao lamanja, ndi pa chala chachikulu cha phazi lao lamanja ndi kuuwaza mwaziwo paguwa la nsembe posungulira.