Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Ahebri 9:20 - Buku Lopatulika

20 nati, Uwu ndi mwazi wa chipangano Mulungu adakulamulani.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

20 nati, Uwu ndi mwazi wa chipangano Mulungu adakulamulani.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

20 Pochita zimenezi adanenerera mau akuti, “Aŵa ndi magazi otsimikizira Chipangano chimene Mulungu walamula kuti mchisunge.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

20 Iye anati, “Awa ndi magazi a pangano limene Mulungu wakulamulirani kuti mulisunge.”

Onani mutuwo Koperani




Ahebri 9:20
6 Mawu Ofanana  

Ndipo Mose anatenga mwaziwo, nawaza pa anthu, nati Taonani mwazi wa chipangano, chimene Yehova anachita nanu, kunena za mau awa onse.


Iwenso, chifukwa cha mwazi wa pangano lako ndinatulutsa andende ako m'dzenje m'mene mulibe madzi.


pakuti ichi ndi mwazi wanga wa pangano wothiridwa chifukwa cha anthu ambiri ku kuchotsa machimo.


kuti mulowe chipangano cha Yehova Mulungu wanu, ndi lumbiriro lake, limene Yehova Mulungu wanu achita ndi inu lero lino;


Koma Mulungu wa mtendere amene anabwera naye wotuluka mwa akufa Mbusa wamkulu wa nkhosa ndi mwazi wa chipangano chosatha, ndiye Ambuye wathu Yesu,


Ndipo zinamuka kwa Yoswa kumisasa ku Giligala, ndipo zinati kwa iye ndi kwa amuna a Israele, Tachokera dziko lakutali, chifukwa chake mupangane nafe.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa