Ahebri 8:7 - Buku Lopatulika7 Pakuti loyamba lija likadakhala lopanda chilema sakadafuna malo a lachiwirilo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Pakuti loyamba lija likadakhala lopanda chilema sakadafuna malo a lachiwirilo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Chipangano choyamba chija chikadakhala changwiro, sipakadafunikanso china m'malo mwake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Ngati pangano loyamba lija likanakhala langwiro, sipakanafunikanso lina mʼmalo mwake. Onani mutuwo |