Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Ahebri 7:23 - Buku Lopatulika

23 Ndipo iwo ndiwo ambiri anakhala ansembe, popeza imfa idawaletsa asakhalebe;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

23 Ndipo iwo ndiwo ambiri anakhala ansembe, popeza imfa idawaletsa asakhalebe;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

23 Kusiyana kwina nkwakuti ansembe akale aja anali ambiri, chifukwa ankafa, sankatha kupitirira ndi udindo waowo.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

23 Tsono ansembe akale aja analipo ambiri, popeza imfa imawalepheretsa kupitiriza ntchitoyi.

Onani mutuwo Koperani




Ahebri 7:23
7 Mawu Ofanana  

Koma Yohane anati amkanize, nanena, Ndiyenera ine kubatizidwa ndi Inu, ndipo Inu mudza kwa ine kodi?


koma Iye ndi lumbiro mwa Iye amene anenana kwa Iye, Walumbira Ambuye ndipo sadzalapa, iwe ndiwe wansembe nthawi yosatha).


Momwemonso Yesu wakhala Nkhoswe ya pangano loposa.


koma Iye chifukwa kuti akhala Iye nthawi yosatha ali nao unsembe wosasinthika,


Ndipo pano anthu ofeka alandira limodzi la magawo khumi; koma apo iye, woti adamchitira umboni kuti ali ndi moyo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa