Ahebri 7:14 - Buku Lopatulika14 Pakuti kwadziwikadi kuti Ambuye wathu anatuluka mwa Yuda; za fuko ili Mose sanalankhule kanthu ka ansembe. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 Pakuti kwadziwikadi kuti Ambuye wathu anatuluka mwa Yuda; za fuko ili Mose sanalankhula kanthu ka ansembe. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Nchodziŵikiratu kuti Ambuye athu aja anali a fuko la Yuda, ndipo Mose pokamba za fuko limeneli, sadanenepo kanthu za ansembe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Pakuti nʼzodziwika bwino kuti Ambuye athu anachokera fuko la Yuda. Kunena za fuko limeneli, Mose sananenepo kanthu za ansembe. Onani mutuwo |