Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Ahebri 5:6 - Buku Lopatulika

6 Monga anenanso mwina, Iwe ndiwe wansembe wa nthawi zonse monga mwa dongosolo la Melkizedeki.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

6 Monga anenanso mwina, Iwe ndiwe wansembe wa nthawi zonse monga mwa dongosolo la Melkizedeki.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

6 Penanso Mulungu adati, “Ndiwe wansembe mpaka muyaya, unsembe wake wonga uja wa Melkizedeki.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

6 Ndipo penanso anati, “Iwe ndiwe wansembe mpaka muyaya, monga mwa unsembe wa Melikizedeki.”

Onani mutuwo Koperani




Ahebri 5:6
10 Mawu Ofanana  

Yehova walumbira, ndipo sadzasintha, Inu ndinu wansembe kosatha monga mwa chilongosoko cha Melkizedeki.


wotchedwa ndi Mulungu mkulu wa ansembe monga mwa dongosolo la Melkizedeki.


m'mene Yesu mtsogoleri analowamo chifukwa cha ife, atakhala mkulu wa ansembe nthawi yosatha monga mwa dongosolo la Melkizedeki.


Ndipo pakadakhala ungwiro mwa unsembe wa Chilevi (pakuti momwemo anthu analandira chilamulo), pakadatsala kusowa kotani kuti auke wansembe wina monga mwa dongosolo la Melkizedeki, wosayesedwa monga mwa dongosolo la Aroni?


Ndipo kwadziwikatu koposa ndithu, ngati auka wansembe wina monga mwa mafanidwe a Melkizedeki,


pakuti amchitira umboni, Iwe ndiwe wansembe nthawi yosatha monga mwa dongosolo la Melkizedeki.


koma Iye ndi lumbiro mwa Iye amene anenana kwa Iye, Walumbira Ambuye ndipo sadzalapa, iwe ndiwe wansembe nthawi yosatha).


wopanda atate wake, wopanda amake, wopanda mawerengedwe a chibadwidwe chake, alibe chiyambi cha masiku ake kapena chitsiriziro cha moyo wake, wofanizidwa ndi Mwana wa Mulungu), iyeyu wakhala wansembe kosalekeza.


Ndipo pano anthu ofeka alandira limodzi la magawo khumi; koma apo iye, woti adamchitira umboni kuti ali ndi moyo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa