Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Ahebri 2:5 - Buku Lopatulika

5 Pakuti sanagonjetsere angelo dziko lilinkudza limene tinenali.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

5 Pakuti sanagonjetsera angelo dziko lilinkudza limene tinenali.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

5 Tikamanena za dziko limene lilikudza, si angelo amene Mulungu adaŵapatsa ulamuliro pa dzikolo.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

5 Mulungu sanapereke kwa angelo ulamuliro wa dziko limene likubwerali, limene ife tikulinena.

Onani mutuwo Koperani




Ahebri 2:5
5 Mawu Ofanana  

Ndipo Uthenga uwu Wabwino wa Ufumu udzalalikidwa padziko lonse lapansi, ukhale mboni kwa anthu a mitundu yonse; ndipo pomwepo chidzafika chimaliziro.


Pakuti pano tilibe mzinda wokhalitsa, komatu tifunafuna ulinkudzawo.


nalawa mau okoma a Mulungu, ndi mphamvu ya nthawi ilinkudza,


Koma monga mwa lonjezano lake tiyembekezera miyamba yatsopano, ndi dziko latsopano m'menemo mukhalitsa chilungamo.


Ndipo mngelo wachisanu ndi chiwiri anaomba lipenga, ndipo panakhala mau aakulu mu Mwamba, ndi kunena, Ufumu wa dziko lapansi wayamba kukhala wa Ambuye wathu, ndi wa Khristu wake: ndipo adzachita ufumu kufikira nthawi za nthawi.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa