Ahebri 2:6 - Buku Lopatulika6 Koma wina anachita umboni pena, nati, Munthu nchiyani kuti mumkumbukira iye? Kapena mwana wa munthu kuti mucheza naye? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Koma wina anachita umboni pena, nati, Munthu nchiyani kuti mumkumbukira iye? Kapena mwana wa munthu kuti mucheza naye? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Koma pena pake wina adanenetsa m'Malembo kuti, “Kodi munthu nchiyani, kuti muzimkumbukira, mwana wa munthu nchiyani, kuti muzimsamala? Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Koma palipo pena pamene wina anachitira umboni kuti, “Kodi munthu ndani kuti muzimukumbukira, kapena mwana wa munthu kuti muzimusamalira? Onani mutuwo |