Ahebri 2:1 - Buku Lopatulika1 Mwa ichi tiyenera kusamaliradi zimene tidazimvazi kuti kapena tingatengedwe ndi kusiyana nazo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Mwa ichi tiyenera kusamaliradi zimene tidazimvazi kuti kapena tingatengedwe ndi kusiyana nazo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Nchifukwa chake tsono, zimene tidamva, tizizisamala kwambiri, kuwopa kuti pang'ono ndi pang'ono tingazitaye. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Nʼchifukwa chake, ife tiyenera kusamalira kwambiri zimene tinamva, kuopa kuti pangʼono ndi pangʼono tingazitaye. Onani mutuwo |