Ahebri 13:6 - Buku Lopatulika6 Kotero kuti tinena molimbika mtima, Mthandizi wanga ndiye Ambuye; sindidzaopa; adzandichitira chiyani munthu? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Kotero kuti tinena molimbika mtima, Mthandizi wanga ndiye Ambuye; sindidzaopa; adzandichitira chiyani munthu? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Tiyeni tsono tilimbe mtima ndi kunena kuti, “Ambuye ndiwo Mthandizi wanga, sindidzachita mantha. Munthu angandichite chiyani?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Kotero ife tikunena molimba mtima kuti, “Ambuye ndiye mthandizi wanga; sindidzachita mantha. Munthu angandichitenji ine?” Onani mutuwo |