Ahebri 13:3 - Buku Lopatulika3 Kumbukirani am'nsinga, monga am'nsinga anzao; ochitidwa zoipa, monga ngati inunso adatero nanu m'thupi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Kumbukirani am'nsinga, monga am'nsinga anzao; ochitidwa zoipa, monga ngati inunso adatero nanu m'thupi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Muzikumbukira am'ndende, ngati kuti mukuzunzikira nawo limodzi m'ndendemo. Muzikumbukira ovutitsidwa, pakuti inunso muli ndi thupi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Muzikumbukira amene ali mʼndende ngati kuti inunso ndi omangidwa, ndiponso amene akusautsidwa ngati inunso mukuvutika. Onani mutuwo |