Ahebri 13:2 - Buku Lopatulika2 Musaiwale kuchereza alendo; pakuti mwa ichi ena anachereza angelo osachidziwa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Musaiwale kuchereza alendo; pakuti mwa ichi ena anachereza angelo osachidziwa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Musanyozere kumalandira bwino alendo m'nyumba mwanu. Pali ena amene kale adaalandira bwino alendo, ndipo mosazindikira adaalandira angelo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Musayiwale kusamalira alendo, pakuti pochita zimenezi anthu ena anasamalira angelo amene samawadziwa. Onani mutuwo |