Ahebri 12:8 - Buku Lopatulika8 Koma ngati mukhala opanda chilango, chimene onse adalawako, pamenepo muli am'thengo, si ana ai. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Koma ngati mukhala opanda chilango, chimene onse adalawako, pamenepo muli am'thengo, si ana ai. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Ngati Mulungu sakulangani inuyo, monga amachitira ndi ana ake onse, ndiye kuti sindinu ana enieni, koma am'chigololo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Ngati inu simulangidwa, komatu aliyense amalangidwa, ndiye kuti sindinu ana enieni koma amʼchigololo. Onani mutuwo |