Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Ahebri 11:2 - Buku Lopatulika

2 Pakuti momwemo akulu anachitidwa umboni.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

2 Pakuti momwemo akulu anachitidwa umboni.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

2 Pokhala ndi chikhulupiriro, makolo anthu akale aja Mulungu adaonetsa kuti ankakondwera nawo.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

2 Ndi chikhulupiriro chimenechi makolo athu akale anayamikidwa.

Onani mutuwo Koperani




Ahebri 11:2
3 Mawu Ofanana  

Kale Mulungu analankhula ndi makolo mwa aneneri m'manenedwe ambiri ndi mosiyanasiyana,


Ndipo iwo onse adachitidwa umboni mwa chikhulupiriro, sanalandire lonjezanolo,


Ndi chikhulupiriro Abele anapereka kwa Mulungu nsembe yoposa ija ya Kaini, imene anachitidwa umboni nayo kuti anali wolungama; nachitapo umboni Mulungu pa mitulo yake; ndipo momwemo iye, angakhale adafa alankhulabe.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa