Ahebri 10:12 - Buku Lopatulika12 koma Iye, m'mene adapereka nsembe imodzi chifukwa cha machimo, anakhala padzanja lamanja la Mulungu chikhalire; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 koma Iye, m'mene adapereka nsembe imodzi chifukwa cha machimo, anakhala pa dzanja lamanja la Mulungu chikhalire; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Koma Khristu adapereka nsembe imodzi yokha yochotsera machimo onse. Ndipo ataipereka, adakakhala ku dzanja lamanja la Mulungu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Koma pamene wansembe uyu anapereka kamodzi kokha nsembe imodzi yokha chifukwa cha machimo, Iye anakhala pansi ku dzanja lamanja la Mulungu. Onani mutuwo |