Ahebri 1:7 - Buku Lopatulika7 Ndipo za angelo anenadi, Amene ayesa angelo ake mizimu, ndi omtumikira Iye akhale malawi amoto. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Ndipo za angelo anenadi, Amene ayesa angelo ake mizimu, ndi omtumikira Iye akhale malawi amoto. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Ndipo za angelo Mulungu adati, “Mulungu amasandutsa angelo ake mphepo, atumiki ake amaŵasandutsa malaŵi a moto.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Iye ponena za angelo akuti, “Mulungu amasandutsa angelo ake mphepo, amasandutsa atumiki ake malawi amoto.” Onani mutuwo |