Afilipi 4:22 - Buku Lopatulika22 Oyera mtima onse akupatsani inu moni, koma makamaka iwo a banja la Kaisara. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201422 Oyera mtima onse alankhula inu, koma makamaka iwo a banja la Kaisara. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa22 Akukupatsani moni anthu onse a Mulungu amene ali kuno, makamakanso ogwira ntchito ku nyumba ya Mfumu ya ku Roma. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero22 Oyera mtima onse akupereka moni, makamaka iwo a ku nyumba ya Kaisara. Onani mutuwo |