Afilipi 4:21 - Buku Lopatulika21 Perekani moni kwa woyera mtima aliyense mwa Khristu Yesu. Abalewo akukhala ndi ine akupatsani moni. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 Lankhulani woyera mtima aliyense mwa Khristu Yesu. Abalewo akukhala ndi ine alankhula inu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 M'dzina la Khristu Yesu mundiperekereko moni kwa aliyense wamumpingo. Akukupatsani moni abale amene ndili nawo pamodzi kuno. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Perekani moni kwa oyera mtima onse mwa Khristu Yesu. Abale amene ali ndi ine akupereka moni wawo. Onani mutuwo |