Afilipi 4:2 - Buku Lopatulika2 Ndidandaulira Yuwodiya, ndidandaulira Sintike, alingirire ndi mtima umodzi mwa Ambuye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Ndidandaulira Yuwodiya, ndidandaulira Sintike, alingirire ndi mtima umodzi mwa Ambuye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Yuwodiyayo ndi Sintikeyo ndaŵapemba, chonde akhale omvana, popeza kuti ndi abale mwa Ambuye. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Ndikudandaulira Euodiya ndi Suntuke kuti akhale ndi mtima umodzi mwa Ambuye. Onani mutuwo |