Afilipi 3:17 - Buku Lopatulika17 Abale, khalani pamodzi akutsanza anga, ndipo yang'anirani iwo akuyenda kotero monga muli ndi ife chitsanzo chanu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 Abale, khalani pamodzi akutsanza anga, ndipo yang'anirani iwo akuyenda kotero monga muli ndi ife chitsanzo chanu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 Abale anga, nonse pamodzi muzinditsanzira ine, ndipo muziŵapenyetsetsa amene amayenda motsata chitsanzo chimene ife timakupatsani. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 Abale, nonsenu pamodzi mudzinditsanzira ine, ndipo monga inu muli ndi chitsanzo, phunzirani kwa amene akukhala moyo motsatira momwe timakhalira. Onani mutuwo |