Afilipi 3:16 - Buku Lopatulika16 chokhachi, kumene tidafikirako, mayendedwe athu alinganeko. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 chokhachi, kumene tidafikirako, mayendedwe athu alinganeko. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Koma ngakhale zitani, tisatayepo kanthu pa zoona zimene takhala tikuzikhulupirira mpaka tsopano. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Tiyeni ife tizikhala mogwirizana ndi zimene tinapeza kale basi. Onani mutuwo |