Afilipi 3:14 - Buku Lopatulika14 ndilondetsa polekezerapo, kutsatira mfupo wa maitanidwe akumwamba a Mulungu a mwa Khristu Yesu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 ndilondetsa polekezerapo, kutsatira mfupo wa maitanidwe akumwamba a Mulungu a mwa Khristu Yesu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Ndikuthamangira ku mapeto a mpikisano wa liŵirowu, kuti ndikalandire mphotho Kumwamba, imene Mulungu akutiitanira kudzera mwa Khristu Yesu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Ndikuthamangira kokathera mpikisanowo kuti ndikalandire mphotho imeneyi kumwamba, imene Mulungu anandiyitanira mwa Khristu Yesu. Onani mutuwo |