Afilipi 2:28 - Buku Lopatulika28 Chifukwa chake ndamtuma iye chifulumizire, kuti pakumuona mukakondwerenso, ndi inenso chindichepere chisoni. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201428 Chifukwa chake ndamtuma iye chifulumizire, kuti pakumuona mukakondwerenso, ndi inenso chindichepere chisoni. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa28 Nchifukwa chake ndikufunitsitsa ndithu kumtumiza kwa inu, kuti podzamuwonanso mudzasangalale, kutinso nkhaŵa yanga ichepeko. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero28 Choncho khumbo langa lofulumiza kumutumiza lakula, kuti pamene mumuonenso musangalale komanso kuti nkhawa yanga ichepe. Onani mutuwo |