Afilipi 2:24 - Buku Lopatulika24 koma ndikhulupirira mwa Ambuye kuti ine ndekhanso ndidzadza msanga. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201424 koma ndikhulupirira mwa Ambuye kuti ine ndekhanso ndidzadza msanga. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa24 Koma ndikhulupirira kuti, Ambuye akalola, inenso ndidzafika kwanuko msanga. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero24 Ndipo ndikukhulupirira kuti Ambuye akalola ine mwini ndidzafikanso kwanuko posachedwapa. Onani mutuwo |