Afilipi 2:23 - Buku Lopatulika23 Ameneyo ndithu tsono ndiyembekeza kumtuma posachedwa m'mene ndikapenyerera za kwa ine zidzatani; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201423 Ameneyo ndithu tsono ndiyembekeza kumtuma posachedwa m'mene ndikapenyerera za kwa ine zidzatani; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa23 Ndikuyembekeza tsono kumtumiza kwa inu msanga, nditadziŵa za m'mene ziyendere zanga. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero23 Choncho ndikuyembekezera kumutuma msanga ndikangodziwa mmene zinthu zanga ziyendere. Onani mutuwo |