Afilipi 2:21 - Buku Lopatulika21 Pakuti onsewa atsata za iwo okha, si za Yesu Khristu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 Pakuti onsewa atsata za iwo okha, si za Yesu Khristu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Paja ena onse amangofuna zokomera iwo okha, osati zokomera Yesu Khristu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Pakuti aliyense amangofuna zokomera iye yekha osati zokomera Yesu Khristu. Onani mutuwo |