Afilipi 2:20 - Buku Lopatulika20 Pakuti ndilibe wina wa mtima womwewo, amene adzasamalira za kwa inu ndi mtima woona. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201420 Pakuti ndilibe wina wa mtima womwewo, amene adzasamalira za kwa inu ndi mtima woona. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa20 Ndilibenso wina wonga amene ali ndi mtima wosamala za inu kwenikweni. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero20 Ndilibenso wina monga iyeyu amene ali ndi chidwi chenicheni pa za moyo wanu. Onani mutuwo |