Afilipi 2:14 - Buku Lopatulika14 Chitani zonse kopanda madandaulo ndi makani, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 Chitani zonse kopanda madandaulo ndi makani, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Muzichita zonse mosanyinyirika ndi mosatsutsapo, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Muzichita zonse mosawiringula kapena mosatsutsapo, Onani mutuwo |