Afilipi 1:21 - Buku Lopatulika21 Pakuti kwa ine kukhala ndi moyo ndiko Khristu, ndi kufa kuli kupindula. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 Pakuti kwa ine kukhala ndi moyo ndiko Khristu, ndi kufa kuli kupindula. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Kwa inetu moyo ndi Khristu amene, ndipo nayonso imfa ili ndi phindu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Pakuti kwa ine kukhala moyo ndi Khristu ndipo kufa ndi phindu. Onani mutuwo |