Aefeso 6:4 - Buku Lopatulika4 Ndipo atate inu, musakwiyitse ana anu; komatu muwalere iwo m'maleredwe ndi chilangizo cha Ambuye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Ndipo atate inu, musakwiyitse ana anu; komatu muwalere iwo m'maleredwe ndi chilangizo cha Ambuye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Inu atate, musamaŵapsetsa mtima ana anu, koma muziŵalera bwino pakuŵasungitsa mwambo ndi malangizo a Ambuye. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Abambo musakwiyitse ana anu; mʼmalo mwake, muwalere mʼchiphunzitso ndi mʼchilangizo cha Ambuye. Onani mutuwo |