Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Aefeso 4:20 - Buku Lopatulika

20 Koma inu simunaphunzire Khristu chotero,

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

20 Koma inu simunaphunzira Khristu chotero,

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

20 Koma umu si m'mene inu mudaphunzirira za Khristu ai,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

20 Koma inu simunadziwe Khristu mʼnjira yotere.

Onani mutuwo Koperani




Aefeso 4:20
8 Mawu Ofanana  

Senzani goli langa, ndipo phunzirani kwa Ine; chifukwa ndili wofatsa ndi wodzichepetsa mtima: ndipo mudzapeza mpumulo wa miyoyo yanu.


ndi kuti kulalikidwe m'dzina lake kulapa ndi kukhululukidwa kwa machimo kwa mitundu yonse, kuyambira ku Yerusalemu.


Chalembedwa mwa aneneri, Ndipo adzakhala onse ophunzitsidwa ndi Mulungu. Yense amene adamva kwa Atate, naphunzira, adza kwa Ine.


ngatitu mudamva Iye, ndipo munaphunzitsidwa mwa Iye, monga choonadi chili mwa Yesu;


Ndipo inu, kudzoza kumene munalandira kuchokera kwa Iye, kukhala mwa inu, ndipo simusowa kuti wina akuphunzitseni; koma monga kudzoza kwake kukuphunzitsani za zinthu zonse, ndipo kuli koona, sikuli bodza ai, ndipo monga kudaphunzitsa inu, mukhale mwa Iye.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa