Aefeso 4:2 - Buku Lopatulika2 ndi kuonetsera kudzichepetsa konse, ndi chifatso, ndi kuonetsera chipiriro, ndi kulolerana wina ndi mnzake, mwa chikondi; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 ndi kuonetsera kudzichepetsa konse, ndi chifatso, ndi kuonetsera chipiriro, ndi kulolerana wina ndi mnzake, mwa chikondi; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Muzikhala odzichepetsa, ofatsa ndi opirira nthaŵi zonse. Muzilezerana mtima mwachikondi, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Mukhale odzichepetsa kwathunthu ndi ofatsa; mukhale oleza mtima, ololerana wina ndi mnzake mwachikondi. Onani mutuwo |