Aefeso 4:10 - Buku Lopatulika10 Iye wotsikayo ndiye yemweyonso anakwera, popitiriratu miyamba yonse, kuti akadzaze zinthu zonse. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Iye wotsikayo ndiye yemweyonso anakwera, popitiriratu miyamba yonse, kuti akadzaze zinthu zonse. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Iye amene adaatsika, ndi yemweyo amene adakwera, nabzola Kumwamba konse, kuti zinthu zonse zikhale zodzaza ndi Iye. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Iye amene anatsika ndi yemweyo anakwera koposa mʼmayiko a kumwamba onse, ndi cholinga choti zinthu zonse zikhale zodzaza ndi Iye. Onani mutuwo |