Aefeso 1:16 - Buku Lopatulika16 sindileka kuyamika chifukwa cha inu, ndi kukumbukira inu m'mapemphero anga; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 sindileka kuyamika chifukwa cha inu, ndi kukumbukira inu m'mapemphero anga; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Nchifukwa chake sindilekeza kuthokoza Mulungu chifukwa cha inu. Ndimakukumbukirani m'mapemphero anga, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 ine sindilekeza kuyamika Mulungu chifukwa cha inu. Ndimakukumbukirani mʼmapemphero anga. Onani mutuwo |