2 Yohane 1:8 - Buku Lopatulika8 Mudzipenyerere nokha, kuti mungataye zimene tazichita, koma kuti mulandire mphotho yokwanira. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Mudzipenyerere nokha, kuti mungataye zimene tazichita, koma kuti mulandire mphotho yokwanira. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Chenjerani kuti mungataye chimene mwagwirira ntchito, koma yesetsani kuti mukalandire mphotho yathunthu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Chenjerani kuti mungataye chimene mwagwirira ntchito, koma chitani khama kuti mukalandire mphotho yanu yonse. Onani mutuwo |