2 Yohane 1:11 - Buku Lopatulika11 Pakuti iye wakumpatsa moni ayanjana nazo ntchito zake zoipa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Pakuti iye wakumpatsa moni ayanjana nazo ntchito zake zoipa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 pakuti wopatsa munthu wotere moni, akuvomereza zochita zake zoipa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Aliyense wolandira munthu wotere ndiye kuti akuvomerezana nazo ntchito zake zoyipa. Onani mutuwo |