2 Yohane 1:10 - Buku Lopatulika10 Munthu akadza kwa inu, wosatenga chiphunzitso ichi, musamlandire iye kunyumba, ndipo musampatse moni. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Munthu akadza kwa inu, wosatenga chiphunzitso ichi, musamlandire iye kunyumba, ndipo musampatse moni. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Wina aliyense akadza kwa inu osaphunzitsa zimenezi, musamlandire m'nyumba mwanu. Musampatse ndi moni womwe, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Ngati wina aliyense abwera kwa inu osaphunzitsa zimenezi, musamulandire mʼnyumba mwanu kapena kumupatsa moni. Onani mutuwo |